Musaweruze kuweruza ndi kwa mwini wake mulungu tsoka kwa amene amanyoza mtumiki wa mulungu, amati sibwino kunyoza mtumiki wa mulungu, kuli bwino kukhala chete chifukwa uti ungotengapo thembelero pa chabe.
Anybody attacking somebody calling upon the name of Jesus Christ is having a problem and needs deliverance. Riches shouldn’t be a reason of calling somebody satanic. Period!
iwe ndi ine ndi osiyana ine ndi madziwa kuti ndiwa Satanic. ndi khululupilira kuti iwenso ndi m’modzi waiw. ndikusambitsani limodzi mwazi wa Yesu khristu
Ndiye nchito yimeyi yaba.
If u want to be rich , be a prophet u can have money so soon , naw call me prophet wilfred Kaimaima kkk
Zonse mulungu akuona
is there any one tell me what prophet mean
Musaweruze kuweruza ndi kwa mwini wake mulungu tsoka kwa amene amanyoza mtumiki wa mulungu, amati sibwino kunyoza mtumiki wa mulungu, kuli bwino kukhala chete chifukwa uti ungotengapo thembelero pa chabe.
they are getting rich on earth while telling us ulemelelo uli ku heaven.
kaya
he just bought a new jet and gotta the sick..sicker
Prophet Shepherd Bushiri a true man of God eyeeeeee!!!
Masiku otsiliza
MAN OF GOD! Wathu wathu wachiMalawi, why not proud of…
Anybody attacking somebody calling upon the name of Jesus Christ is having a problem and needs deliverance. Riches shouldn’t be a reason of calling somebody satanic. Period!
There is no such a Godamme creature called a prophet,but there is one called a crook!
Put the word PROPHET in inverted comas cos there is no such a thing!
Za Satanic zo kkkkkkk
Kaya Bushiri Ndiwasatanic Kaya Ayi Km Zonse Amadziwa Ndimulungu Osati Iwe.
iwe ndi ine ndi osiyana ine ndi madziwa kuti ndiwa Satanic. ndi khululupilira kuti iwenso ndi m’modzi waiw. ndikusambitsani limodzi mwazi wa Yesu khristu